Miyambo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukapanda kumvera, udzabuula kumapeto kwa moyo wako,Mphamvu zako zikadzatha komanso ukadzawonda kwambiri.+
11 Ukapanda kumvera, udzabuula kumapeto kwa moyo wako,Mphamvu zako zikadzatha komanso ukadzawonda kwambiri.+