Miyambo 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Imwa madzi ochokera mʼchitsime chako,Komanso madzi oyenderera kuchokera pakasupe wako.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:15 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 30