Miyambo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiye mwana wanga, kodi pali chifukwa chilichonse choti uzisangalalira ndi mkazi wamakhalidwe oipa,*Kapena choti uzikumbatirira chifuwa cha mkazi wachiwerewere?*+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:20 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 30
20 Ndiye mwana wanga, kodi pali chifukwa chilichonse choti uzisangalalira ndi mkazi wamakhalidwe oipa,*Kapena choti uzikumbatirira chifuwa cha mkazi wachiwerewere?*+