Miyambo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uchite izi mwana wanga kuti udzipulumutse,Chifukwa uli mʼmanja mwa mnzako: Pita ukadzichepetse ndipo ukamuchonderere kwambiri mnzakoyo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:3 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,9/15/2000, ptsa. 25-267/15/1991, tsa. 27
3 Uchite izi mwana wanga kuti udzipulumutse,Chifukwa uli mʼmanja mwa mnzako: Pita ukadzichepetse ndipo ukamuchonderere kwambiri mnzakoyo.+