Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mboni yachinyengo imene nthawi zonse imanena mabodza,+Komanso aliyense amene amayambitsa mikangano pakati pa abale.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:19 Nsanja ya Olonda,9/15/2000, tsa. 2710/15/1989, tsa. 204/15/1987, tsa. 17
19 Mboni yachinyengo imene nthawi zonse imanena mabodza,+Komanso aliyense amene amayambitsa mikangano pakati pa abale.+