Miyambo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu osadziwa zinthu, phunzirani kukhala ochenjera.+Opusa inu, khalani ndi mtima womvetsa zinthu.* Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda,3/15/2001, tsa. 26