Miyambo 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine nzeru, ndimakhala pamodzi ndi kuchenjera.Ndimadziwa zinthu ndiponso ndimatha kuganiza bwino.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:12 Nsanja ya Olonda,3/15/2001, ptsa. 26-27