Miyambo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zimene munthu amapeza kwa ine nʼzabwino kuposa golide, ngakhale golide woyengedwa bwino kwambiri,Ndipo mphatso zimene ndimapereka nʼzabwino kuposa siliva wabwino kwambiri.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:19 Nsanja ya Olonda,3/15/2001, ptsa. 27-28
19 Zimene munthu amapeza kwa ine nʼzabwino kuposa golide, ngakhale golide woyengedwa bwino kwambiri,Ndipo mphatso zimene ndimapereka nʼzabwino kuposa siliva wabwino kwambiri.+