Miyambo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu amene amabisa chidani mumtima mwake amalankhula mabodza,+Ndipo amene amafalitsa mphekesera zoipa ndi wopusa. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:18 Nsanja ya Olonda,9/15/2001, tsa. 25
18 Munthu amene amabisa chidani mumtima mwake amalankhula mabodza,+Ndipo amene amafalitsa mphekesera zoipa ndi wopusa.