Miyambo 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kukhulupirika kwa anthu owongoka mtima nʼkumene kumawatsogolera,+Koma wochita zinthu mwachinyengo adzawonongedwa chifukwa cha mabodza ake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:3 Nsanja ya Olonda,5/15/2002, tsa. 26
3 Kukhulupirika kwa anthu owongoka mtima nʼkumene kumawatsogolera,+Koma wochita zinthu mwachinyengo adzawonongedwa chifukwa cha mabodza ake.+