Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chuma chidzakhala chopanda* phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+Koma chilungamo nʼchimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:4 Nsanja ya Olonda,5/15/2002, tsa. 26
4 Chuma chidzakhala chopanda* phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+Koma chilungamo nʼchimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+