Miyambo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilungamo cha munthu wopanda cholakwa chimawongola njira yake,Koma woipa adzagwa chifukwa cha kuipa kwake komwe.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:5 Nsanja ya Olonda,5/15/2002, tsa. 26
5 Chilungamo cha munthu wopanda cholakwa chimawongola njira yake,Koma woipa adzagwa chifukwa cha kuipa kwake komwe.+