Miyambo 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wampatuko* amawononga mnzake ndi pakamwa pake,Koma anthu olungama amapulumutsidwa chifukwa chodziwa zinthu.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:9 Nsanja ya Olonda,5/15/2002, tsa. 26
9 Wampatuko* amawononga mnzake ndi pakamwa pake,Koma anthu olungama amapulumutsidwa chifukwa chodziwa zinthu.+