Miyambo 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense wopanda nzeru amasonyeza kuti akuipidwa ndi* mnzake,Koma munthu amene alidi wozindikira amakhala chete.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:12 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, tsa. 55/15/2002, tsa. 273/15/1997, ptsa. 12-13
12 Aliyense wopanda nzeru amasonyeza kuti akuipidwa ndi* mnzake,Koma munthu amene alidi wozindikira amakhala chete.+