Miyambo 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakakhala popanda malangizo anzeru, anthu amagwa.Koma zinthu zimayenda bwino* ngati pali alangizi* ambiri.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:14 Nsanja ya Olonda,5/15/2002, ptsa. 27-28
14 Pakakhala popanda malangizo anzeru, anthu amagwa.Koma zinthu zimayenda bwino* ngati pali alangizi* ambiri.+