Miyambo 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene amalonjeza kuti adzapereka ngongole ya munthu wachilendo mwiniwakeyo akadzalephera kubweza, zinthu sizidzamuyendera bwino.+Koma amene amapewa* kugwirana dzanja pochita mgwirizano adzakhala wotetezeka. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:15 Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 28
15 Munthu amene amalonjeza kuti adzapereka ngongole ya munthu wachilendo mwiniwakeyo akadzalephera kubweza, zinthu sizidzamuyendera bwino.+Koma amene amapewa* kugwirana dzanja pochita mgwirizano adzakhala wotetezeka.