Miyambo 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wosasunthika pachilungamo adzapeza moyo,+Koma munthu wofunafuna zoipa adzafa.