Miyambo 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zimene munthu wolungama amalakalaka zimakhala ndi zotsatira zabwino.+Koma zimene oipa amayembekezera zimabweretsa mkwiyo woopsa.
23 Zimene munthu wolungama amalakalaka zimakhala ndi zotsatira zabwino.+Koma zimene oipa amayembekezera zimabweretsa mkwiyo woopsa.