Miyambo 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amapereka mowolowa manja* ndipo pamapeto pake amakhala ndi zinthu zochuluka.+Munthu wina amaumira zimene amafunika kupatsa anthu ena, koma amasauka.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:24 Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 30
24 Munthu amapereka mowolowa manja* ndipo pamapeto pake amakhala ndi zinthu zochuluka.+Munthu wina amaumira zimene amafunika kupatsa anthu ena, koma amasauka.+