Miyambo 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu amene amafunitsitsa kuchita zabwino, adzakomeredwa mtima.+Koma wofunitsitsa kuchita zoipa, zoipazo zidzamʼbwerera.+
27 Munthu amene amafunitsitsa kuchita zabwino, adzakomeredwa mtima.+Koma wofunitsitsa kuchita zoipa, zoipazo zidzamʼbwerera.+