Miyambo 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aliyense wobweretsa mavuto* kwa anthu amʼbanja lake cholowa chake chidzakhala mphepo,+Ndipo munthu wopusa adzakhala wantchito wa munthu wanzeru. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:29 Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 31
29 Aliyense wobweretsa mavuto* kwa anthu amʼbanja lake cholowa chake chidzakhala mphepo,+Ndipo munthu wopusa adzakhala wantchito wa munthu wanzeru.