Miyambo 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pali munthu amene amadzionetsa ngati wolemera koma chonsecho alibe chilichonse.+Pali munthu winanso amene amadzionetsa ngati wosauka koma ali ndi chuma chambiri. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:7 Nsanja ya Olonda,9/15/2003, tsa. 23
7 Pali munthu amene amadzionetsa ngati wolemera koma chonsecho alibe chilichonse.+Pali munthu winanso amene amadzionetsa ngati wosauka koma ali ndi chuma chambiri.