Miyambo 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chuma chimene munthu amachipeza mofulumira* sichichedwa kutha,+Koma chuma cha munthu amene wachipeza pangʼonopangʼono* chidzawonjezeka. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Nsanja ya Olonda,9/15/2003, tsa. 25
11 Chuma chimene munthu amachipeza mofulumira* sichichedwa kutha,+Koma chuma cha munthu amene wachipeza pangʼonopangʼono* chidzawonjezeka.