Miyambo 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense amene safuna kutsatira malangizo, adzakumana ndi mavuto chifukwa cha zochita zakezo,+Koma munthu amene amamvera malamulo adzalandira mphoto.+
13 Aliyense amene safuna kutsatira malangizo, adzakumana ndi mavuto chifukwa cha zochita zakezo,+Koma munthu amene amamvera malamulo adzalandira mphoto.+