Miyambo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼnyumba ya munthu wolungama muli chuma chambiri,Koma zokolola za munthu woipa zimamubweretsera mavuto.+
6 Mʼnyumba ya munthu wolungama muli chuma chambiri,Koma zokolola za munthu woipa zimamubweretsera mavuto.+