Miyambo 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu wopeza phindu mwachinyengo amabweretsa mavuto* kwa anthu amʼbanja lake,+Koma amene amadana ndi ziphuphu adzakhalabe ndi moyo.+
27 Munthu wopeza phindu mwachinyengo amabweretsa mavuto* kwa anthu amʼbanja lake,+Koma amene amadana ndi ziphuphu adzakhalabe ndi moyo.+