Miyambo 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kupeza nzeru nʼkwabwino kwambiri kuposa kupeza golide.+ Ndipo ndi bwino kusankha kumvetsa zinthu kuposa siliva.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:16 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, tsa. 8
16 Kupeza nzeru nʼkwabwino kwambiri kuposa kupeza golide.+ Ndipo ndi bwino kusankha kumvetsa zinthu kuposa siliva.+