Miyambo 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu owongoka mtima amapewa kuchita zinthu zoipa. Aliyense amene amateteza njira yake, amasunga moyo wake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:17 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, tsa. 8
17 Anthu owongoka mtima amapewa kuchita zinthu zoipa. Aliyense amene amateteza njira yake, amasunga moyo wake.+