Miyambo 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wa mtima wanzeru adzatchedwa wozindikira,+Ndipo amene amalankhula mokoma mtima* amakopa ena ndi mawu akewo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:21 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, ptsa. 9-10
21 Munthu wa mtima wanzeru adzatchedwa wozindikira,+Ndipo amene amalankhula mokoma mtima* amakopa ena ndi mawu akewo.+