Miyambo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndi bwino kudya mkate wouma pali mtendere,*+Kusiyana ndi kuchita maphwando ochuluka* mʼnyumba imene muli mikangano.+
17 Ndi bwino kudya mkate wouma pali mtendere,*+Kusiyana ndi kuchita maphwando ochuluka* mʼnyumba imene muli mikangano.+