Miyambo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zidzukulu zili ngati chisoti chaulemu kwa anthu okalamba,Ndipo ana amalemekezeka chifukwa cha bambo awo.* Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:6 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
6 Zidzukulu zili ngati chisoti chaulemu kwa anthu okalamba,Ndipo ana amalemekezeka chifukwa cha bambo awo.*