Miyambo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wopusa sasangalala ndi kumvetsa zinthu.Iye amangokonda kuulula zimene zili mumtima mwake.+