Miyambo 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu woipa akabwera, pamabweranso kunyozeka,Ndipo munthu akamachita zinthu zochititsa manyazi amanyozeka.+
3 Munthu woipa akabwera, pamabweranso kunyozeka,Ndipo munthu akamachita zinthu zochititsa manyazi amanyozeka.+