Miyambo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu ambiri amafuna kukondedwa ndi munthu wolemekezeka,*Ndipo aliyense ndi bwenzi la munthu wopereka mphatso.
6 Anthu ambiri amafuna kukondedwa ndi munthu wolemekezeka,*Ndipo aliyense ndi bwenzi la munthu wopereka mphatso.