Miyambo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,Ndipo amene amalankhula zabodza zokhazokha adzawonongedwa.+