Miyambo 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu waulesi amapisa dzanja lake mʼmbale ya chakudya,Koma nʼkulephera kulibweretsa pakamwa.+