Miyambo 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Miyala yachinyengo* yoyezera ndi yonyansa kwa Yehova,Ndipo masikelo achinyengo si abwino.