Miyambo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ukakhala pansi kuti udye ndi mfumu,Uzionetsetsa zimene zili pamaso pako.