-
Miyambo 23:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Chifukwa iye ali ngati munthu amene amakuyangʼanitsitsa kuti adziwe kuchuluka kwa chakudya chimene wadya.
Iye amakuuza kuti: “Idya ndi kumwa,” koma salankhula zimenezo ndi mtima wonse.
-