-
Miyambo 23:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndi ndani amene akuvutika? Ndi ndani amene ali ndi nkhawa?
Ndi ndani amene ali pa mikangano? Ndi ndani amene ali ndi madandaulo?
Ndi ndani amene ali ndi mabala popanda chifukwa? Ndi ndani amene ali ndi maso ofiira?
-