Miyambo 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yengani siliva nʼkuchotsa zonse zosafunika,Ndipo yense adzatuluka woyengeka bwino.+