Miyambo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Thetsa nkhaniyo pokambirana ndi mnzakoyo,+Koma usaulule nkhani zachinsinsi zimene unauzidwa,*+