Miyambo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera+Amakhala ngati ndolo yagolide ndiponso ngati chokongoletsera chagolide woyenga bwino. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:12 Nsanja ya Olonda,12/15/1997, tsa. 32
12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera+Amakhala ngati ndolo yagolide ndiponso ngati chokongoletsera chagolide woyenga bwino.