Miyambo 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu wodzitama kuti apereka mphatso koma nʼkulephera kupereka,+Ali ngati mitambo komanso mphepo yosabweretsa mvula.
14 Munthu wodzitama kuti apereka mphatso koma nʼkulephera kupereka,+Ali ngati mitambo komanso mphepo yosabweretsa mvula.