Miyambo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopereka umboni wabodza pa mlandu wa mnzake+Ali ngati chibonga chakunkhondo, lupanga, komanso muvi wakuthwa.
18 Munthu wopereka umboni wabodza pa mlandu wa mnzake+Ali ngati chibonga chakunkhondo, lupanga, komanso muvi wakuthwa.