Miyambo 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wolungama amene amagonja* nʼkuchita zofuna za munthu woipaAmakhala ngati kasupe wamatope komanso chitsime chimene chawonongedwa.
26 Munthu wolungama amene amagonja* nʼkuchita zofuna za munthu woipaAmakhala ngati kasupe wamatope komanso chitsime chimene chawonongedwa.