Miyambo 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Si bwino kudya uchi wambiri,+Komanso si bwino kuti munthu adzifunire yekha ulemerero.+