Miyambo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Sinowo sayenera kugwa mʼchilimwe ndiponso mvula siyenera kugwa pa nthawi yokolola,Chimodzimodzinso munthu wopusa, iye sayenera kulemekezedwa.+
26 Sinowo sayenera kugwa mʼchilimwe ndiponso mvula siyenera kugwa pa nthawi yokolola,Chimodzimodzinso munthu wopusa, iye sayenera kulemekezedwa.+