Miyambo 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu amene amasiya ntchito yake mʼmanja mwa munthu wopusaAli ngati munthu amene wapundula mapazi ake nʼkudzivulaza yekha.* Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:6 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 30
6 Munthu amene amasiya ntchito yake mʼmanja mwa munthu wopusaAli ngati munthu amene wapundula mapazi ake nʼkudzivulaza yekha.*