Miyambo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kupereka ulemerero kwa munthu wopusa,+Kuli ngati kumanga mwala pagulaye.*